mutchenetse by Malawi Artist - Malawi music
Malawi Music

mutchenetse

2026 03:04 MalawiSongs
Listen

mutchenetse by Malawi Artist

nyimboyi ikulimbikitsa amuna omwe akuganiza zosiya akazi awo chifukwa chakuti asiya kuoneka bwino ndipo awona ena akunja omwe akuvala bwino komaso kusamalika bwino, ndipo ikuwalimbikitsa kuti mkazi wao yemweyi akuoneka kuipatu angathe kumujudura ndikumaonekaso kuwala mmene iwo akufunira

Discover Malawi Music

Explore more Malawi music on MalawiSongs. Browse new Malawi songs and trending songs from Malawian artists.